Bzalani mtedza mvula yoyamba ikagwa yokwanira. Bzalanai mtedza pampata oyenera kuti mukolole zochuluka.