Zulani tsangwe imodzi kuti muone ngati mtedza wakhwima. Kumbani mtedza panthawi yake kuti mtedzawo usaphulike, usakhalire m’nthaka komanso usagwidwe ndi chuku. Umitsani mtedza mukamaliza kukumba