Module Articles

Nzama

Nzama

Kusankha Malo

Nzama zimakula bwino pa nthaka yophatikizana ndi mchenga omwe uli ndi mchere ochuluka komaso manyowa ochepekera ndi dothi losunga madzi. Bzalani nzama motsatana chimanga pa ulimi wakasinthasintha. Bzalani nzama mwakasakaniza ndi mbewu zina monga chimanga ndi chinangwa.

Sosani munda pogwiritsa ntchito chotchetchera, khasu ndi leki. Galauzani munda masabata awiri musanabzale pogwiritsa ntchito khasu ndi leki.