Nsabwe (aphids) – poperani mankhwala a Dimethoate.
Matenda a nzama
Wilt Sclerotium blight (Sclerotium rolfsii) (chiwawu) ndi Leaf spot (cercospora canescens) – bzalani mwansanga, mwakasinthasintha ndi kupopera mankhwala.