Za eMlimi

eMlimi ndi upangili wamakono omwe umapezeka mumafoni amakono, Upangiliwu Olumikizitsa ogula mbewu, alimi ndi ena kuti apindule ndi zokolora zomwe zasokhanisidwa pa modzi muno Mmalawi komanso kupititsa patsogolo mauthenga a ulimi amakono , za misika yambewu, za nyengo komanso zamadyedwe abwino oyenela ndi zinazambili

e-MLILMI
e-MLILMI

Timapeleka
Upangili wazawulimi

Gawo lamawuthenga aza mbewu olembedwa mwawukadawulo ndi owelengedwa bwino komanso kupeza misika.Gawo laza upangili wakalimidwe kamakono ndi chakudya chomwe ife amalawi timadalira upititsidwa pastogolo ndicholinga choti tizikhala ndichakudya chokwanila komanso zakudya zamagulu onse

Katundu Waulimi

Kmpani yogulitsa katundu/Ogulitsa osakhazikika

Pa eMlimi mbali yazamisika, Mwaena Ogula mbewu adalembetsa. eMlimi amasunga mayina anthu ogula mbewu ndi mayina makampani ogula mbewu omwe adalembetsa ndima manambala afoni ndimbewu zomwe amagula kwa alimi.

fresh products

Total Volumes Traded

5,569,883
kgs

Total Value Traded

3,209,691,168.00
MKW

Agritrading

Saniyani
Malonda ngavaulimi

  • Kachewere

    Chindewe

    1500kg @
    MKW2000

  • Kachewere

    Chindewe

    1000kg @
    MKW2000

  • Chimanga

    Chapulapula

    5000kg @
    MKW1500

  • Ulimi Wa Nsomba

    Chapulapula

    5000kg @
    MKW1500

  • Kachewere

    Chimbwanda

    420kg @
    MKW1300

  • Kachewere

    Chimbwanda

    620kg @
    MKW1500

Kutenga kuchokera pa intaneti

eMlimi App

Our app is available on Google Play Store! Download now to get started!

Mobile App

Incorporated by