eMlimi ndi upangili wamakono omwe umapezeka mumafoni amakono, Upangiliwu Olumikizitsa ogula mbewu, alimi ndi ena kuti apindule ndi zokolora zomwe zasokhanisidwa pa modzi muno Mmalawi komanso kupititsa patsogolo mauthenga a ulimi amakono , za misika yambewu, za nyengo komanso zamadyedwe abwino oyenela ndi zinazambili