Module Articles

Nzama

Nzama

Kubzala

Bzalani nzama pamene mvula yagwa bwino mwezi wa October kufikira December pa mizere yotalikirana 75cm kapena 90cm komanso 15 cm kutalikirana kwa mapando. Bzalani 100kg mpaka 110kg pa hekitala.  Thirani inoculant pobzala.