zulani mbewu zonse zosafunikira m’munda. Palirani ndi makasu mtedza usanayambe kuyika. Zulani ndi manja popalira ngati mtedza wayamba maluwa kuti musasokoneze mizu. Mungathe kugwiritsa ntchito mankhwala opha udzu.