Sungani misisi ya Ginger kwa miyezi yosachepera iwiri kapena itatu kuchokera patsiku lokololera kuti ikadzalidwenso. Mitsitsi ya Ginger ikhoza kusungidwa poyika mumasamba ndi kusunga padothi.