Munda wa Ginger uyenera kuphimbidwa ndi masamba ndi cholinga chosunga chinyezi ndi kuonjezera manyowa zikawola.
Munda wa Ginger uyenera kuthiriridwa pafupipafupi ndi cholinga chosunga chinyezi.
Munda wa Ginger uyenera kuthiridwa manyowa osakaniziridwa bwino pa mulingo wa 5kg kapena 10Kg pa bed lililonse.