Munda olima ginger uyenera kukhala wabwino, okonzedwa bwino ndiponso osalazidwa bwino. Misisi imeneyi ikhoza kudzalidwa mabedi kapena mizere. Mamebi ayenera kukhala 120cm mu litali ndi 20cm mpaka 25cm mu lifupi.