Module Articles
Tomato
Tomato
Kukolola
Kukolola
- Thyolani tomato wanu pamene wayamba kumene kupsa kuti muyende naye bwino mtunda wa utali.
Kasungidwe
- Sungani tomato mmalo ouma, ozizira bwino ndi odutsa mphepo. Asakhale onyowa
- Tomato yense wosweka kapena wamabala ayikidwe payekha
- Sankhani tomato molingana ndi kukula komanso maonekedwe ake kuti mugulitse mtengo wabwino.