Module Articles

Mpunga

Mpunga

Kasamalidwe ka zokolola

  • Dulani mpunga pamene wacha. Punthani mpunga kuti ulekane ndi mtengo wake. Petani mpunga kuti muchotse mphwemphwa ndi zinyalala. Yanikani mpunga pamalo abwino kuti uume. Sungani mpunga mmatumba ukauma