Konzani nazale yabwino komanso mu nthawi yoyenera kuti mbewu ifesedwe ndi kuokeledwa msanga. Nazale iyenela kukhala yotalika 20m mulitali ndi 1m mulifupi ndipo kuchoka pansi kufika pamwamba iyenela kukhala 5cm
Kubzala
Bzalani mbande za mpunga mmapando pogwiritsa ntchito manja kapena makina.
Wazani mbewu ya mpunga ndi kusakaniza ndi dothi pogwiritsa ntchito pulawo kapena halo. Meletsani mbewu ya mpunga isanakaokeredwe mmpapando nthawi ya chilimwe.
Bzalani mbewu 6 pa phando lililonse lotalikilana ndilizake 23cm x 23cm