Module Articles

Maphunziro Okonzekera Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi Ndi Covaca

Maphunziro Okonzekera Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi Ndi Covaca

Mau Otsogolera

  • Ngakhale tigwire ntchito zodziteteza/ mavuto ogwa mwadzidzidzi azichitikabe// Kumvetsetsa Za Tsatane-tsatane wokonzekera/ kuchepetsa ndi kupewa Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi//
  • Tikuyenera kukonzekera mavutowa kuti tidzathe kuchitapo kanthu mwadongosolo//
  • Ntchito yochepetsa mavuto ogwa mwadzidzidzi/ ikuyenelanso kupititsa patsogolo ntchito zachitukuko//
  • Ndipo tiwonetsetse kuti anthu/ asakhale ndimtima wodalira katundu wolandira