Module Articles

Maphunziro Okonzekera Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi Ndi Covaca

Maphunziro Okonzekera Ngozi Zogwa Mwadzidzidzi Ndi Covaca

Ngodya za EWS

Phindu logwilitsa Ntchito EWS

  1. Zizindikilozi zimathathandiza kuchepetsa kutaya chuma/ chiwelengelo cha anthu omwe angavulal/ komanso imfa – anthu amadziwitsidwa ndi kupanga zoti aziteteze iwowo ndi katundu wawo.
  2. Zimawathandizila anthu/ powakhonzekeleketsa komanso kuchitapo kanthu ngozizi Anthu amachita zofunika pa nthawi yoyenelera pomwe zisanachitike//
  3.  

Zitsanso za zipangizo zochecheza anthu ku ngozi zogwa mwadzidzidiz/Mdern/scientific Early Warning Systems

Three colored

Level 1 green:Alert/Standby/Ready-Level 2, yellow: Preparation “Get Set”-Level 3: Evacuation-Red

 

Water level gauges.

 

Rain gauge

 

Traditional dissemination system