Mlimi ayenera kusankha mbewu yovomerezeka yogwirizana ndi dera lomwe akukhala kuti tizipeza phindu lochuluka.
Mitundu ya mbewu; Chimanga cha Hybrid ndi OBV (chimanga cha masika)