Chimanga
Ulimi Wa Nsomba
Kukolola
- Sengani chimanga ndikuchiika pa mkuku kuti chimalizike kuuma moyenera. (njirayi ndiyothandiza chifukwa mumakolola mosavuta)
- Chotsani chimanga ku mapesi pogwiritsa ntchito manja.
- Tonolani chimanga ndikupeta musanaike mosungiramo
- Sungani moyenera pothira mankhwala a Actellic kuti chisafumbwe
- Sungani muzipangizo zoyenera monga nkhokwe zovomerezeka kapena mmatumba.