Gulu la S4T ndi gulu lomwe amagwilizana anthu oyambila pa 10 kufikila pa 25 amsonkhana ndalama pamodzi kenanko ndikuamtenga ngongole zing'onozing'ono. S4T imekhalapo kwa miyezi khumi ndi iwir (12) kapena kuti chaka chimodzi kenako amagawana ndalama zonse ndikuyambilanso chaka china. Gulu la S4T limatsogozedwa ndi anthu eni ake amene alimgululo osati alngizi akumudzi omwe amawaphunzitsa kapena alangizi olembedwa ntchito a Boma kapena mabungwe.
Ntchito yophunzitsa magulu a S4T imakhala mmanja a Mphunzitsi wakumuzi (S4T Promoter) kapena Voluntiya amene bungwe la World Vision limamusula ngati kaswili wamaphunzilo. Uyu ndi munthu amene salipidwa chilichonse kupatulako thandizo limene gulu lingmupatse mwakufuna kwawo pothokoza chifukwa chantchito yake. Aphunzitsi akumudzi amayenela kukhala membala wagulu la S4T mdela lawo. Ntchito za Mlangizi wakumuzdzi ndi izi: