Module Articles

Kusunga Ndi Kubwerekana Ndalama M'njila Yosintha Miyoyo

Kusunga Ndi Kubwerekana Ndalama M'njila Yosintha Miyoyo

Chitsanzo cha kugawana ndalama

S4T yotchedwa Kamoza mmuzi wa Kawuwaili ndi mamembala 10,  amene amagula sheyapamtengo wa  MK100.00, ndipo pakutha kwachaka apeza K280,000.00 yoti agawane Chaka chitatha ndondomeko yawo ili choncho:-

Dzina

Sheya/gawo

Sheys imodzi

Ndalama zonse

 

Grace Banda

100

K200.00

MK20,000.00

 

Andrew Mbewe

200

K200.00

MK40,000.00

 

Bension Qoto

50

K200.00

MK10,000.00

 

Hense Ndhlovu

200

K200.00

MK40,000.00

 

Albert Nyirenda

300

K200.00

MK60,000.00

 

Grey Mphande

80

K200.00

MK16,000.00

 

Bright Chavula

150

K200.00

MK30,000.00

 

Laston Honde

20

K200.00

MK40,00.00

 

Jessie Gondwe

200

K200.00

MK40,000.00

 

Sweke Jere

100

K200.00

MK20,000.00

 

Zonse

1400

 

MK280,000.00

 

 

Ndalama zomwe munthu angalandire:-

                        MK280,000.00/1400  =  MK200.00  yimene tipange matiply kapena kuyichulukitsa ndi ma sheya amuunthu.